Salimo 78:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye anatulutsa madzi ambiri pathanthwe,+Ndipo anachititsa madzi kutsika ngati mitsinje.+ Yesaya 48:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo sanamve ludzu+ ngakhale pamene iye anawayendetsa m’chipululu.+ Iye anawatulutsira madzi pathanthwe. Anang’amba thanthwe kuti madzi atulukepo.”+
21 Iwo sanamve ludzu+ ngakhale pamene iye anawayendetsa m’chipululu.+ Iye anawatulutsira madzi pathanthwe. Anang’amba thanthwe kuti madzi atulukepo.”+