1 Mbiri 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Yamikani Yehova,+ anthu inu. Itanani pa dzina lake.+Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake!+ Salimo 136:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 136 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino:+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
136 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino:+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+