Salimo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+ Salimo 146:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye ndi Woperekera chiweruzo anthu ochitiridwa chinyengo,+Wopereka chakudya kwa anthu anjala.+Yehova amamasula anthu omangidwa.+ Yeremiya 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova. Luka 1:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Wakhutitsa anthu anjala ndi zinthu zabwino,+ amene anali ndi chuma wawapitikitsa chimanjamanja.+
10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+
7 Iye ndi Woperekera chiweruzo anthu ochitiridwa chinyengo,+Wopereka chakudya kwa anthu anjala.+Yehova amamasula anthu omangidwa.+
14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova.