3 Popeza kuti analibe bambo, analibe mayi, analibe mzere wa mibadwo ya makolo ndipo tsiku limene anabadwa+ komanso limene anamwalira silikudziwika, koma anamuchititsa kuti afanane ndi Mwana wa Mulungu,+ iye ndi wansembe kwamuyaya.+
11 Ndiyeno, ngati zikanakhala zothekadi kuti munthu akhale wangwiro+ kudzera mu unsembe wa Alevi,+ kodi pakanafunikanso kuti pakhale wansembe wina+ monga mwa unsembe wa Melekizedeki+ osati monga mwa unsembe wa Aroni? (Unsembe wa Alevi unali mbali ya Chilamulo pamene chinaperekedwa kwa anthu.)+