Oweruza 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,+Dziko linagwedezeka,+ kumwamba kunagwetsa madzi,+Mitambo inagwetsa madzi. Ezekieli 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Ine ndidzalankhula mwaukali wanga+ woyaka moto komanso nditakwiya kwambiri.+ Ndithudi, pa tsikulo m’dziko la Isiraeli mudzachitika chivomezi chachikulu.+ Hagai 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Posachedwapa+ ndigwedezanso kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndi mtunda.’+
4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,+Dziko linagwedezeka,+ kumwamba kunagwetsa madzi,+Mitambo inagwetsa madzi.
19 ‘Ine ndidzalankhula mwaukali wanga+ woyaka moto komanso nditakwiya kwambiri.+ Ndithudi, pa tsikulo m’dziko la Isiraeli mudzachitika chivomezi chachikulu.+
6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Posachedwapa+ ndigwedezanso kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndi mtunda.’+