Deuteronomo 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a m’badwo woipa uwu amene adzaona dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+ Deuteronomo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Mwana wako akadzakufunsa tsiku lina m’tsogolo+ kuti, ‘Kodi zikumbutso, malangizo ndi zigamulo izi zimene Yehova Mulungu wathu anakupatsani, zimatanthauza chiyani?’ Salimo 105:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+
35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a m’badwo woipa uwu amene adzaona dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+
20 “Mwana wako akadzakufunsa tsiku lina m’tsogolo+ kuti, ‘Kodi zikumbutso, malangizo ndi zigamulo izi zimene Yehova Mulungu wathu anakupatsani, zimatanthauza chiyani?’
5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+