Salimo 119:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kwadzaza dziko lonse lapansi.+Ndiphunzitseni malamulo anu.+ Yesaya 48:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu, amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,+ amene ndimakuchititsani kuti muyende m’njira imene muyenera kuyendamo.+ Yohane 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+ Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+
64 Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kwadzaza dziko lonse lapansi.+Ndiphunzitseni malamulo anu.+
17 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu, amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,+ amene ndimakuchititsani kuti muyende m’njira imene muyenera kuyendamo.+
45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+