Salimo 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova ndiye gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa,+ komanso chikho changa.+Inu mukundisungira bwino kwambiri cholowa changa. Salimo 73:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Thupi langa ndi mtima wanga zalefuka.+Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga ndiponso cholowa changa mpaka kalekale.+ Yeremiya 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Mulungu wa Yakobo+ sali ngati mafanowa. Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Isiraeli ndiye ndodo ya cholowa chake.+ Dzina la Mulunguyo ndi Yehova wa makamu.+
5 Yehova ndiye gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa,+ komanso chikho changa.+Inu mukundisungira bwino kwambiri cholowa changa.
26 Thupi langa ndi mtima wanga zalefuka.+Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga ndiponso cholowa changa mpaka kalekale.+
16 Koma Mulungu wa Yakobo+ sali ngati mafanowa. Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Isiraeli ndiye ndodo ya cholowa chake.+ Dzina la Mulunguyo ndi Yehova wa makamu.+