Deuteronomo 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko mudzatumikira milungu+ yopangidwa ndi manja a anthu, milungu ya mtengo ndi mwala,+ imene siingaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.+ Salimo 115:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mafano awo ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+
28 Kumeneko mudzatumikira milungu+ yopangidwa ndi manja a anthu, milungu ya mtengo ndi mwala,+ imene siingaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.+