Salimo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndinaitana inu Yehova,+Ndipo ndinachonderera Yehova kuti andikomere mtima.+ Salimo 77:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Ndidzafuulira Mulungu,+Ndithu, ndidzafuulira Mulungu, ndipo iye adzatchera khutu lake kwa ine.+ Salimo 141:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 141 Inu Yehova, ine ndakuitanani.+Bwerani kwa ine mofulumira.+Tcherani khutu pamene ndikukuitanani.+