Salimo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti muweruze mwana wamasiye komanso woponderezedwa.+Mudzatero kuti munthu wamba wochokera kufumbi asachititsenso anthu ena kunjenjemera.+ Salimo 104:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+
18 Kuti muweruze mwana wamasiye komanso woponderezedwa.+Mudzatero kuti munthu wamba wochokera kufumbi asachititsenso anthu ena kunjenjemera.+
15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+