Salimo 117:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale.Tamandani Ya, anthu inu!+ Chivumbulutso 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya, anthu inu!+ Utsi wochokera kwa iye udzafuka kwamuyaya.”+
2 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale.Tamandani Ya, anthu inu!+
3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya, anthu inu!+ Utsi wochokera kwa iye udzafuka kwamuyaya.”+