2 Mbiri 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akalonga onse+ ndi anthu onse anayamba kusangalala,+ ndipo anali kubweretsa ndalama za msonkhowo n’kumaziponya m’bokosi+ lija kufikira aliyense anapereka. Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+ Salimo 119:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzakutamandani ndi mtima wowongoka,+Pamene ndikuphunzira zigamulo zanu zolungama.+
10 Akalonga onse+ ndi anthu onse anayamba kusangalala,+ ndipo anali kubweretsa ndalama za msonkhowo n’kumaziponya m’bokosi+ lija kufikira aliyense anapereka.
8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+