Salimo 111:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 111 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Ndidzatamanda Yehova ndi mtima wanga wonse,+ב [Behth]Pakati pa gulu+ la owongoka mtima ndi pamsonkhano wawo.+
111 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Ndidzatamanda Yehova ndi mtima wanga wonse,+ב [Behth]Pakati pa gulu+ la owongoka mtima ndi pamsonkhano wawo.+