Yobu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inenso ndikanatha kulankhula ngati mmene mukuchitiramu,Moyo wanu ukanakhala ngati mmene ulili moyo wanga,Kodi ndikanalankhula mawu ogometsa okunenani?+Ndipo kodi ndikanakupukusirani mutu?+ Salimo 44:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwatisandutsa mwambi pakati pa anthu a mitundu ina,+Mwatisandutsa anthu amene anthu a mitundu inawo akuwapukusira mitu.+ Salimo 109:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kwa iwo ndakhala chinthu choyenera kutonzedwa.+Akandiona amapukusa mitu yawo.+ Mateyu 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano anthu odutsa anayamba kunena mawu onyoza+ Yesu. Anali kupukusa+ mitu yawo
4 Inenso ndikanatha kulankhula ngati mmene mukuchitiramu,Moyo wanu ukanakhala ngati mmene ulili moyo wanga,Kodi ndikanalankhula mawu ogometsa okunenani?+Ndipo kodi ndikanakupukusirani mutu?+
14 Mwatisandutsa mwambi pakati pa anthu a mitundu ina,+Mwatisandutsa anthu amene anthu a mitundu inawo akuwapukusira mitu.+