Salimo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Opani Yehova, inu oyera ake,+Pakuti onse omuopa sasowa kanthu.+ Salimo 84:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+ Mateyu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+ Afilipi 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nayenso Mulungu wanga+ adzakupatsani zosowa zanu zonse+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake+ chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu. Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+
11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+
33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+
19 Nayenso Mulungu wanga+ adzakupatsani zosowa zanu zonse+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake+ chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu.
5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+