Deuteronomo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Adzaitanira mitundu ya anthu kuphiri.Kumeneko adzapereka nsembe zachilungamo.+Pakuti adzayamwa chuma chochuluka cha m’nyanja,+Ndi chuma chobisika cha mumchenga.” Salimo 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukatero mudzakondwera ndi nsembe zachilungamo,+Mudzakondwera ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zathunthu.+Pamenepo ng’ombe zamphongo zidzaperekedwa paguwa lanu la nsembe.+
19 Adzaitanira mitundu ya anthu kuphiri.Kumeneko adzapereka nsembe zachilungamo.+Pakuti adzayamwa chuma chochuluka cha m’nyanja,+Ndi chuma chobisika cha mumchenga.”
19 Mukatero mudzakondwera ndi nsembe zachilungamo,+Mudzakondwera ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zathunthu.+Pamenepo ng’ombe zamphongo zidzaperekedwa paguwa lanu la nsembe.+