Yesaya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amene ali ndi mtima wosagwedezeka mudzawateteza powapatsa mtendere wosatha,+ chifukwa amadalira inu.+ Aroma 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Paja Lemba limati: “Palibe wokhulupirira iye,+ amene adzakhumudwe.”+
3 Anthu amene ali ndi mtima wosagwedezeka mudzawateteza powapatsa mtendere wosatha,+ chifukwa amadalira inu.+