Salimo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chitani zimenezi kuti mdani wanga asanene kuti: “Ndamugonjetsa!”Kutinso adani anga asakondwere chifukwa chakuti ine ndadzandira.+ Salimo 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+ Salimo 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukatero ndidziwa kuti mwasangalala nane,Chifukwa mdani wanga sadzafuula mosangalala kuti wandipambana.+
4 Chitani zimenezi kuti mdani wanga asanene kuti: “Ndamugonjetsa!”Kutinso adani anga asakondwere chifukwa chakuti ine ndadzandira.+
19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+
11 Mukatero ndidziwa kuti mwasangalala nane,Chifukwa mdani wanga sadzafuula mosangalala kuti wandipambana.+