Genesis 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Yehova anati: “Kodi ndingamubisire Abulahamu zimene ndikufuna kuchita?+ Miyambo 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti munthu wochita zachiphamaso+ Yehova amanyansidwa naye,+ koma amakonda anthu owongoka mtima.+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+ Yohane 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sindikutchanso inu kuti akapolo, chifukwa kapolo sadziwa zimene mbuye wake amachita. Koma ndakutchani mabwenzi,+ chifukwa zonse zimene ndamva kwa Atate wanga ndakudziwitsani.+
32 Pakuti munthu wochita zachiphamaso+ Yehova amanyansidwa naye,+ koma amakonda anthu owongoka mtima.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
15 Sindikutchanso inu kuti akapolo, chifukwa kapolo sadziwa zimene mbuye wake amachita. Koma ndakutchani mabwenzi,+ chifukwa zonse zimene ndamva kwa Atate wanga ndakudziwitsani.+