Salimo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndimadana ndi olambira mafano opanda pake ndi achabechabe.+Koma ine ndimadalira Yehova.+ Salimo 139:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu kwambiri,+Ndipo anthu okupandukirani ndimanyansidwa nawo.+
21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu kwambiri,+Ndipo anthu okupandukirani ndimanyansidwa nawo.+