Salimo 69:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo ine mtumiki wanu musandibisire nkhope yanu.+Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndasautsika kwambiri.+ Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+ Yesaya 59:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+
17 Ndipo ine mtumiki wanu musandibisire nkhope yanu.+Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndasautsika kwambiri.+
7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+