-
Yesaya 50:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
50 Yehova wanena kuti: “Kodi anthu inu, chili kuti chikalata chothetsera ukwati+ wa mayi wanu yemwe ndinamuthamangitsa?+ Kapena kodi anthu inu ndakugulitsani+ kwa munthu uti amene ndinali naye ngongole? Inutu mwagulitsidwa chifukwa cha zolakwa zanu,+ ndipo mayi wanu wathamangitsidwa chifukwa cha zochimwa zanu.+
-