Salimo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndikuitana inu Yehova.+Inu Thanthwe langa, musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana,+Kuti musakhale chete pamaso panga,+Kutinso ine ndisafanane ndi amene akutsikira kudzenje la manda.+ Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+ Yona 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinatsikira m’tsinde mwenimweni mwa mapiri.Zotsekera za dziko lapansi zinanditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.*Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa m’dzenje ndili wamoyo.+
28 Ndikuitana inu Yehova.+Inu Thanthwe langa, musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana,+Kuti musakhale chete pamaso panga,+Kutinso ine ndisafanane ndi amene akutsikira kudzenje la manda.+
17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+
6 Ndinatsikira m’tsinde mwenimweni mwa mapiri.Zotsekera za dziko lapansi zinanditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.*Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa m’dzenje ndili wamoyo.+