Salimo 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+ Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+ Mlaliki 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+ Yakobo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 inu mumasangalala ndi wovala zapamwamba uja+ ndipo mumamuuza kuti: “Khalani pamalo pabwinopa,” koma kwa wosauka uja mumati: “Imirira choncho,” kapena: “Khala pansipa pafupi ndi chopondapo mapazi anga.”
11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+
8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+
15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+
3 inu mumasangalala ndi wovala zapamwamba uja+ ndipo mumamuuza kuti: “Khalani pamalo pabwinopa,” koma kwa wosauka uja mumati: “Imirira choncho,” kapena: “Khala pansipa pafupi ndi chopondapo mapazi anga.”