Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Salimo 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsiku lililonse amakomera mtima ena ndi kuwakongoza zinthu,+Ndipo ana ake adzalandira madalitso.+ Machitidwe 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pakuti lonjezoli+ laperekedwa kwa inu, kwa ana anu ndi kwa onse akutali,+ onse amene Yehova Mulungu wathu angawasankhe.”+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
39 Pakuti lonjezoli+ laperekedwa kwa inu, kwa ana anu ndi kwa onse akutali,+ onse amene Yehova Mulungu wathu angawasankhe.”+