Miyambo 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 pakuti chuma sichidzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo chisoti chachifumu sichidzakhalapo ku mibadwo yonse. Mlaliki 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wosonkhanitsa+ anati: “Zachabechabe! Zinthu zonse n’zachabechabe.”+
24 pakuti chuma sichidzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo chisoti chachifumu sichidzakhalapo ku mibadwo yonse.