Miyambo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha nzeru.+ Kudziwa Woyera Koposa, ndiko kumvetsa zinthu.+ Mlaliki 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+ Mlaliki 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndani angafanane ndi munthu wanzeru?+ Ndipo ndani amadziwa kumasulira zinthu?+ Nzeru za munthu zimachititsa nkhope yake kuwala ndipo ngakhale nkhope yake yokwiya imasintha n’kumaoneka bwino.+ Akolose 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chuma chonse chokhudzana ndi nzeru ndiponso kudziwa zinthu+ chinabisidwa mosamala mwa iye.
12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+
8 Ndani angafanane ndi munthu wanzeru?+ Ndipo ndani amadziwa kumasulira zinthu?+ Nzeru za munthu zimachititsa nkhope yake kuwala ndipo ngakhale nkhope yake yokwiya imasintha n’kumaoneka bwino.+