Mika 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+ Mateyu 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi inunso, pamaso pa anthu, mumaonekadi ngati olungama+ koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo.
2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+
28 Mofanana ndi zimenezi inunso, pamaso pa anthu, mumaonekadi ngati olungama+ koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo.