Salimo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Miyambo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Woyenda mosalakwa adzapulumutsidwa,+ koma woyenda m’njira zokhota adzagwa mwadzidzidzi.+
21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+