Mlaliki 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chiyambi cha mawu a m’kamwa mwake ndi uchitsiru,+ ndipo mapeto a mawu a m’kamwa mwake ndi misala yomvetsa chisoni. Mateyu 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino, pamene muli oipa?+ Pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+ Yakobo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu.
13 Chiyambi cha mawu a m’kamwa mwake ndi uchitsiru,+ ndipo mapeto a mawu a m’kamwa mwake ndi misala yomvetsa chisoni.
34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino, pamene muli oipa?+ Pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+
5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu.