Yobu 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngati ndayesa golide chinthu chodalira,Kapena ngati ndanena kwa golide kuti, ‘Ndimadalira iwe,’+ Mlaliki 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+ Luka 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+
12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+
19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+