Numeri 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Likhale pangano la unsembe kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale,+ chifukwa sanalekerere zoti anthu azipikisana ndi Mulungu wake,+ ndiponso waphimba machimo a ana a Isiraeli.’”+ 2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ Miyambo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nzeru zimamanga banja la munthu,+ ndipo kuzindikira kumachititsa kuti lilimbe kwambiri.+ Mateyu 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+
13 Likhale pangano la unsembe kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale,+ chifukwa sanalekerere zoti anthu azipikisana ndi Mulungu wake,+ ndiponso waphimba machimo a ana a Isiraeli.’”+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+