Salimo 128:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti udzadya zipatso za ntchito ya manja ako.+Udzakhala wodala ndipo zinthu zidzakuyendera bwino.+ Miyambo 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu amene amalima munda wake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+ ndipo amene amafunafuna zinthu zopanda phindu adzakhala ndi umphawi waukulu.+ Aefeso 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wakubayo asabenso,+ koma agwire ntchito molimbikira. Agwire ndi manja ake ntchito yabwino,+ kuti akhale ndi kanthu kena kopatsa munthu wosowa.+
2 Pakuti udzadya zipatso za ntchito ya manja ako.+Udzakhala wodala ndipo zinthu zidzakuyendera bwino.+
19 Munthu amene amalima munda wake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+ ndipo amene amafunafuna zinthu zopanda phindu adzakhala ndi umphawi waukulu.+
28 Wakubayo asabenso,+ koma agwire ntchito molimbikira. Agwire ndi manja ake ntchito yabwino,+ kuti akhale ndi kanthu kena kopatsa munthu wosowa.+