Miyambo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense wopusa amanyoza malangizo* a bambo ake,+ koma munthu aliyense womvera chidzudzulo ndi wochenjera.+ Aheberi 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+
5 Aliyense wopusa amanyoza malangizo* a bambo ake,+ koma munthu aliyense womvera chidzudzulo ndi wochenjera.+
7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+