Miyambo 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aliyense wokana malangizo+ amakana moyo wake, koma munthu womvetsera chidzudzulo amakhala ndi mtima wanzeru.+ Aheberi 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Samalani kuti musasiye kumvetsera wolankhulayo.+ Pakuti ngati amene analephera kumvera wopereka chenjezo la Mulungu padziko lapansi sanapulumuke,+ kuli bwanji ifeyo? Nafenso sitidzapulumuka tikachoka kwa iye amene amalankhula ali kumwamba.+
32 Aliyense wokana malangizo+ amakana moyo wake, koma munthu womvetsera chidzudzulo amakhala ndi mtima wanzeru.+
25 Samalani kuti musasiye kumvetsera wolankhulayo.+ Pakuti ngati amene analephera kumvera wopereka chenjezo la Mulungu padziko lapansi sanapulumuke,+ kuli bwanji ifeyo? Nafenso sitidzapulumuka tikachoka kwa iye amene amalankhula ali kumwamba.+