Yesaya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+ Aroma 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma aliyense wochita zabwino,+ choyamba Myuda+ kenako Mgiriki,+ adzalandira ulemerero, ulemu ndi mtendere.
10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+
10 Koma aliyense wochita zabwino,+ choyamba Myuda+ kenako Mgiriki,+ adzalandira ulemerero, ulemu ndi mtendere.