Nehemiya 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mfumu inati: “N’chifukwa chiyani nkhope yako ili yachisoni+ pamene sukudwala? Pali chinachake chimene chikukuvutitsa mumtima.”+ Atanena zimenezi ndinachita mantha kwambiri. Salimo 143:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga+ walefuka,Ndipo wachita dzanzi.+ Miyambo 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhawa mumtima mwa munthu ndi imene imauweramitsa,+ koma mawu abwino ndi amene amausangalatsa.+
2 Ndiyeno mfumu inati: “N’chifukwa chiyani nkhope yako ili yachisoni+ pamene sukudwala? Pali chinachake chimene chikukuvutitsa mumtima.”+ Atanena zimenezi ndinachita mantha kwambiri.