Miyambo 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kuopa Yehova ndiko chitsime cha moyo,+ chifukwa kumateteza moyo kumisampha ya imfa.+ Miyambo 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Njira ya kumoyo ndi yowongoka kwa munthu wochita zanzeru,+ kuti asatsikire pansi ku Manda.+ Yohane 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma amene adzamwa madzi amene ine ndidzam’patse sadzamvanso ludzu m’pang’ono pomwe.+ Ndipo madzi amene ndidzam’patse, adzasanduka kasupe wa madzi+ otuluka mwa iye, opatsa moyo wosatha.”+
14 Koma amene adzamwa madzi amene ine ndidzam’patse sadzamvanso ludzu m’pang’ono pomwe.+ Ndipo madzi amene ndidzam’patse, adzasanduka kasupe wa madzi+ otuluka mwa iye, opatsa moyo wosatha.”+