2 Samueli 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+ Mateyu 26:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Atafika, Yudasi analunjika kwa Yesu n’kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu Rabi!”+ Ndipo anam’psompsona.+
31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+
49 Atafika, Yudasi analunjika kwa Yesu n’kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu Rabi!”+ Ndipo anam’psompsona.+