Yeremiya 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 N’chifukwa chiyani ndinabadwa?+ Kodi ndinabadwa kuti ndidzagwire ntchito yakalavulagaga ndi kukhala wachisoni,+ ndi kuti moyo wanga ufike kumapeto kwake ndili wamanyazi?+ Luka 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa masiku akubwera pamene anthu adzanena kuti, ‘Odala ndi akazi osabereka, amene sanaberekepo, komanso amene mabere awo sanayamwitsepo!’+
18 N’chifukwa chiyani ndinabadwa?+ Kodi ndinabadwa kuti ndidzagwire ntchito yakalavulagaga ndi kukhala wachisoni,+ ndi kuti moyo wanga ufike kumapeto kwake ndili wamanyazi?+
29 Chifukwa masiku akubwera pamene anthu adzanena kuti, ‘Odala ndi akazi osabereka, amene sanaberekepo, komanso amene mabere awo sanayamwitsepo!’+