Mlaliki 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndaona ntchito imene Mulungu wapatsa ana a anthu kuti azigwira.+ Mlaliki 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ineyo ndaona ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama ndiponso imene amaigwira bwino,+ kuti imabweretsa mpikisano pakati pa anthu.*+ Izinso n’zachabechabe ndipo zili ngati kuthamangitsa mphepo.
4 Ineyo ndaona ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama ndiponso imene amaigwira bwino,+ kuti imabweretsa mpikisano pakati pa anthu.*+ Izinso n’zachabechabe ndipo zili ngati kuthamangitsa mphepo.