3 Chimene chimamvetsa chisoni pa zinthu zonse zimene zimachitika padziko lapansi pano n’chakuti, popeza mapeto a anthu onse ndi amodzi,+ mtima wa ana a anthu ndi wodzazanso ndi zoipa.+ Mumtima mwawo mumakhala misala+ pa nthawi imene ali ndi moyo ndipo pamapeto pake, iwo amapita kwa akufa.+