-
Chivumbulutso 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nyenyezi zakumwamba zinagwera kudziko lapansi, ngati mmene mkuyu wogwedezeka ndi mphepo yamphamvu umagwetsera nkhuyu zake zosapsa.
-