Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+ Salimo 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo kumwamba kukunena za chilungamo chake,+Pakuti Mulungu ndiye Woweruza.+ [Seʹlah.] Salimo 75:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndiye woweruza.+Amatsitsa wina ndi kukweza wina.+ Salimo 98:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+
25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+
9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+