Luka 24:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndipo pa maziko a dzina lake, m’mitundu yonse+ mudzalalikidwa za kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Kuyambira ku Yerusalemu+ Aroma 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo angalalikire bwanji ngati sanatumidwe?+ Zili monga muja Malemba amanenera kuti: “Mapazi a anthu olengeza uthenga wabwino wa zinthu zabwino, ndi okongola kwabasi!”+
47 ndipo pa maziko a dzina lake, m’mitundu yonse+ mudzalalikidwa za kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Kuyambira ku Yerusalemu+
15 Ndipo angalalikire bwanji ngati sanatumidwe?+ Zili monga muja Malemba amanenera kuti: “Mapazi a anthu olengeza uthenga wabwino wa zinthu zabwino, ndi okongola kwabasi!”+