Yobu 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithudi, mzimu wa anthuNdiponso mpweya wa Wamphamvuyonse n’zimene zimawachititsa kumvetsa zinthu.+ Salimo 147:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ambuye wathu ndi wamkulu ndipo ali ndi mphamvu zochuluka.+Nzeru zake zilibe malire.+
8 Ndithudi, mzimu wa anthuNdiponso mpweya wa Wamphamvuyonse n’zimene zimawachititsa kumvetsa zinthu.+