Salimo 65:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo anthu okhala m’madera akutali adzachita mantha ndi zizindikiro zanu,+Mudzachititsa kulowa ndi kutuluka kwa dzuwa kufuula mokondwera.+ Salimo 66:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muuzeni Mulungu kuti: “Ntchito zanu ndi zochititsadi mantha!+Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zanu, adani anu adzabwera kwa inu mogonjera.+ Salimo 67:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu adzatidalitsa,+Ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzamuopa.+
8 Ndipo anthu okhala m’madera akutali adzachita mantha ndi zizindikiro zanu,+Mudzachititsa kulowa ndi kutuluka kwa dzuwa kufuula mokondwera.+
3 Muuzeni Mulungu kuti: “Ntchito zanu ndi zochititsadi mantha!+Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zanu, adani anu adzabwera kwa inu mogonjera.+