Yeremiya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+ Hoseya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+ Sanamufunefune ngakhale kuti achita zinthu zonsezi.+ Mika 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu anthu anga,+ ndakulakwirani chiyani? Kodi ndakutopetsani mwa njira yanji?+ Perekani umboni wonditsutsa.+
5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+
10 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+ Sanamufunefune ngakhale kuti achita zinthu zonsezi.+
3 “Inu anthu anga,+ ndakulakwirani chiyani? Kodi ndakutopetsani mwa njira yanji?+ Perekani umboni wonditsutsa.+