Yesaya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “M’tsiku limenelo, pamalo alionse pamene panali mitengo ya mpesa 1,000, yokwana ndalama zasiliva 1,000,+ padzakhala tchire la zitsamba zaminga ndi udzu.+ Yesaya 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Panthaka ya anthu anga, pakungomera zitsamba zaminga.+ Zamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo. Zamera m’tauni imene kale inali yodzaza ndi chikondwerero.+ Aheberi 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ikatulutsa minga ndi mitula, imakanidwa ndipo imatsala pang’ono kutembereredwa.+ Mapeto ake imatenthedwa.+
23 “M’tsiku limenelo, pamalo alionse pamene panali mitengo ya mpesa 1,000, yokwana ndalama zasiliva 1,000,+ padzakhala tchire la zitsamba zaminga ndi udzu.+
13 Panthaka ya anthu anga, pakungomera zitsamba zaminga.+ Zamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo. Zamera m’tauni imene kale inali yodzaza ndi chikondwerero.+
8 Koma ikatulutsa minga ndi mitula, imakanidwa ndipo imatsala pang’ono kutembereredwa.+ Mapeto ake imatenthedwa.+